Koma Ichi歌词由DESHO演唱,出自专辑《Koma Ichi》,下面是《Koma Ichi》完整版歌词!
Koma Ichi歌词完整版
Oh yeah yeah yeah
Desho man once again
Chuluke chuluke inded ndiwanjuchi
Umanena yomwe yakuluma
Ndasiya kulira kuwona zokhoma
Chifukwa Cha chikondi chako chokoma
Sindimadziwa ndingamupeze
Mkazi wokongola ngati iwe eeeh
Sindimadziwa ndingamupeze
Mkazi wokonda ngati iwe
Oh my oh my my baby oh my
Oh my oh my my baby
Unkachedwa kuti weeh
Unali kuti honey
Ndichikondi chakochi
Unkachedwa kuti
Ndichikondi chako chokoma
Chikondi koma ichi
Kwina kuja ndinkangochedwa
Chikondi koma ichi
Kwina kuja ndinkadzichedwetsa
Oh yeah yeah
Zokwiyakwiya si mbali yako
Baby ndisaname
Zomveramverazi si mbali yako
Baby ndisaname
Akanakhala wina
Bwez atathawa kale
Zinthuso zikavuta
Ndiwe amene undilimbitsa mtima
Oh my oh my my baby oh my
Oh my oh my my baby
Unkachedwa kuti weeh
Unali kuti honey
Ndichikondi chakochi
Unkachedwa kuti
Ndichikondi chako chokoma
Chikondi koma ichi
Kwina kuja ndinkangochedwa
Chikondi koma ichi
Kwina kuja ndinkadzichedwetsa
Oh yeah yeah
Koma ichi
Chikondi koma ichichi
Koma ichi
Chikondi koma ichichi
Koma ichi
Koma ichi
Chokoma ichi
Chikondi koma ichichi
(Unali kuti honey
Ndichikondi chakochi
Unkachedwa kuti
Ndichikondi chako chokoma
Chikondi koma ichi
Kwina kuja ndinkangochedwa
Chikondi koma ichi
Kwina kuja ndinkadzichedwetsa
Oh yeah yeah)
Ah yeah yeah
Desho Desho
Ah yeah
Tricky eeh
Vikweshekweshe
Iih yeah eh eeh aah yeah yeah yeah