Duwa歌词由Ebel&DJ Sai&Gaxy bo演唱,出自专辑《Duwa》,下面是《Duwa》完整版歌词!
Duwa歌词完整版
Yeah
Dj sai
Me again
Ebel
Yeah iwe ndi duwa losafota
Uli ngat kaganja kosapota
Ndapenga nawe moti ndili zomba
Mental ndakwera instrumental
Ndigula plot mumtima mwakomo
Sindikufuna kupeya rent
Ndimamukonda for real
Sizongopanga pretend
Chikondi chathu cha daily
1 mpaka month end
Kuwala kwako ndi one
Our love will never end
I will treat good
Baeb sudzasowa food
Ndikuthokazi sizandudu
Sinzakuthira makhatcha majudu
Ndikuthokazi sizandudu
Sinzakuthira makhatcha majudu
Ndiwe wokongola ngati kaduwa
Sindikuyimva ndikutengera paguwa
Tabwera tabwera iwe honey taponya sitepe
Ngakhale ma hater aname sindingakuleke
Ndiwe future future future ya ine
Ndiwe dzuwa lowalira dziko la ine
Oyesa kulanda kumusiyira dzino
Kumuluma ngat chi vampaya
Osasekera kumgwira pa khosi
Kumusenda ngat chi pampaya
Chikndi timachifera ngat mtembo
Kuzerezeka nacho ngat bengo
Ndi mmene unakongolera
Or chitsiru chikhoza kukhala ndi mphamvu
Kuwala kwako ndi chiletso mami
Mkazi wa nzeru ndasankha iwe honey
Kusiya iwe ndingalowere kwani
Sindizalora kukudyetsa nkhwani
Ife timakhalana tisapange zibwana
Palibe kusiyana palibe zomenyana
Ndiwe wokongola ngati kaduwa
Sindikuyimva ndikutengera paguwa
Tabwera tabwera iwe honey taponya sitepe
Ngakhale ma hater aname sindingakuleke
Ndiwe future future future ya ine
Ndiwe dzuwa lowalira dziko la ine
Ndiwe wokongola ngati kaduwa
Sindikuyimva ndikutengera paguwa
Tabwera tabwera iwe honey taponya sitepe
Ngakhale ma hater aname sindingakuleke
Ndiwe future future future ya ine
Ndiwe dzuwa lowalira dziko la ine