Bongo (Explicit)歌词由J killz&Cagz演唱,出自专辑《Bongo (Explicit)》,下面是《Bongo (Explicit)》完整版歌词!
Bongo (Explicit)歌词完整版
huu huuh
You're already know!
Achibale amandi ipisa
Ineyo zimandi wawa!
Pitepite ngati njuchi
Tikusakila zokoma chimandi wawa!
Sewenzesa chabe bongo kuti upeze che ma kwacha
Umoyo okoma sumabwela weka
Sewenzesa chabe nzelu kuti upeze chema kwacha
Umoyo okoma sumabwela weka
Gula gula ndikumwele maninga nimwela zanga!
Umoyo okoma sumabwela weka!
Sewenzesa chabe nzelu kuti upeze chema kwacha
Umoyo okoma sumabwela weka
Liyose kukacha all about the starter
Am always a lot yeah ku boba nisiya nakhoma
Udabwa ninveka chitonga suzibza nichoka ku choma yeah
Waziba tachoka patali kufika pano chilenga nichikwama money!
Guy ni plain yeah chita fast lamadani yeah hustle apa ndiye khani
Ngati sikhani ya ndlama we done naka issue kako nika chani apa economy ndiye ili bad
No time nabana mayadi we hustle is what how we're living
Nina 16 call me lagey mabine pali money sunga niteke nfine
No njomba but ndise bamwine pa weekend tiblaka ndlama zabene
Khala wise productive yeah khalako bad madayiva
Chosapo mantha pa hustle mune uzakasala no cash mune
Pa ngako olo zale mu day
Ulina bongo baza mune
Not vachongo whatever I say your boy cags in the truck to day
Pitepite ngati njuchi
Tikusakila zokoma chimandi wawa!
Sewenzesa chabe bongo kuti upeze che ma kwacha
Umoyo okoma sumabwela weka
Sewenzesa chabe nzelu kuti upeze chema kwacha
Umoyo okoma sumabwela weka
Gula gula ndikumwele maninga nimwela zanga!
Umoyo okoma sumabwela weka!
Sewenzesa chabe nzelu kuti upeze chema kwacha
Umoyo okoma sumabwela weka
Yeah oooh umoyo okoma sumabwela weka
Year oooh sumabwela weka
Youre already know yah sumabwela weka