Ukananena歌词由PAYMO MW演唱,出自专辑《Ukananena》,下面是《Ukananena》完整版歌词!
Ukananena歌词完整版
Hook
Bola ukananena kuti sumanvetsetseka
Bola ukananena umakwiya ndikuseka
Bola ukananena ndiwovuta komanso ophweka
Bola ukananena nkanayesa kachikena
Bola ukana mmhuu Bola ukananena (moyo bola ukananena)
Bola ukana mmhuu Bola ukananena (moyo bola ukananena)
Ves 1
Bola ukananena kuti kumbali amandikamba
Nkanadula mtengo sinkanakwezamo kamba
Bola ukananena kuti awa sazinzanga
Ondikonda chifukwa ndili nkandalama (ndili mka dollar)
Ukananena zawachikondi uja
Pamaso ofasa mtima kundizuza
Naye ankangofuna kundidyera kundi user
Dollar zanga zatha taona wabanduka
Ukanena zachikondi sizindipindulira
Ndikanapeza zina Pano zikundipindulira
Osati zama heart break kukusiya ukulira
Bola za money zimakusintha nkumafilla
Hook
Bola ukananena kuti sumanvetsetseka
Bola ukananena umakwiya ndikuseka
Bola ukananena ndiwovuta komanso ophweka
Bola ukananena nkanayesa kachikena
Bola ukana mmhuu Bola ukananena (moyo bola ukananena)
Bola ukana mmhuu Bola ukananena (moyo bola ukananena)
Ves 2
Bola ukananena ndikupanga sizotheka
Sinkana user zonse ndikana user theka (mkana user theka)
Kotsala kusunga kakanabweletsa kena
Bola ukananena bwenzi pano ndili pena
Ukananena ntchito kutsogolo izavuta
Mabanja maudolo zonse zizashupha
Wa Geri or no Geri tonse kuyiphula
Wa mpingo Kaya siwampingo dollar kuyigwira
Ukananena ukakhala mphawi abale amasowa
Amvekere iwe ndi m'bale ukati wachitola
Ukananena andale kuti alibe phindu
Akusangalalala ndiwo Ife dairy kudyera mpilu