Andikonda (Original)歌词由Synord演唱,出自专辑《Andikonda (Original)》,下面是《Andikonda (Original)》完整版歌词!
Andikonda (Original)歌词完整版
ANDIKONDA
V1
Ndapeza bwenzi langa la pa mtima
Bwenzi la pa mtima panga ndi Yesuyo
Za mavuto anga sawerenga andikondabe
Mu nyengo ya zovuta zanga
Ndapeza wa chikondi wanga wanga
Mwana wa Mulungu ine ndasankha
Ndingavutike ndi umphawi andisungabe
Popeza kwa iye ndi ine ofunika
Andipatsa chimwemwe nthawi ya mavuto
Poti andikonda
Andikonda ineyo ooooh
Andipatsa mtendere ndikataya abale
Poti andikonda
Yesu andikonda ineyo oooh (x2)
Talalalalala Talalalalala Talalalalala lala aaaah (x2)
V2
Chikondi chosatha chili mwa Yesu
Ndililiranji ine ndivutikiranji ndi bwenzi la mdziko
Bwenzi la mdziko likhumudwitsa lililitsaaaaaa
Nthawi ya umphawi silionekanso
Mdima ukagwa Yesu alipo adzetsa kuwala
Andidzadza ndi chimwemwe chosatha
Ndavomereza ndizatsata yesu nthawi zonse
Popeza mnyumba ya Mulungu muli mtendere
Andipatsa chimwemwe nthawi ya mavuto
Poti andikonda
Andikonda ineyo ooooh
Andipatsa mtendere ndikataya abale
Poti andikonda
Yesu andikonda ineyo oooh (x2)
Everywhere that I go
It’s your love that I feel inside
Though sometimes I misbehave
It’s my desire to be your son
LORD I need in my life you know that I doooooooo
Andipatsa chimwemwe nthawi ya mavuto
Poti andikonda
Andikonda ineyo ooooh
Andipatsa mtendere ndikataya abale
Poti andikonda
Yesu andikonda ineyo oooh (x2)