Ndimangofuna Ungondilora歌词由DESHO演唱,出自专辑《Ndimangofuna Ungondilora》,下面是《Ndimangofuna Ungondilora》完整版歌词!
Ndimangofuna Ungondilora歌词完整版
Tricky ayee
Eeeeh
Desho Desho
Zoona zake ndiwe wokongola
Ndipo ulusi umawusosola
Kuwona kwanu kweko nkwa ndalama
Kuwona level yako yapamwamba
I have been lying lying lying to you
I have been lying lying lying to you
Zoti ndine Nurse doctor ayee
Ndinkangokamba for you to accept
Ntchito yanga yeniyeni ndiyokolopa
Ntchito yanga yeniyeni ndiyosesa
Zonse zija ine nkangokamba
Ncholinga choti iweyo uvomere
Oh wuh woh oh oh
Ndimangofuna ungondilora
Ndimangofuna ukhale wanga
Ndimangofuna ungondilora
Nchifukwa chake nnakunamiza
Ndimangofuna ungondilora
Ndimangofuna ukhale wanga
Ndimangofuna ungondilora
Nchifukwa chake nnakunamiza
I used to buy things from my friends
To make you comfortable and impressed
Nnayiwala kuti chowuluka chimatera
Nkhani zobisika zija wazitolera
Besides the lie I told you
Ayeee Eeeh
You are the one I want I loooo I care
Ntchito yanga ndiyokolopa
Ntchito yanga ndiyosesa
Ntchito yanga ndiyotchetcha
Ndimangofuna undilore
Undilore iwe undilore
Oh wuh woh oh oh
Ndimangofuna ungondilora
Ndimangofuna ukhale wanga
Ndimangofuna ungondilora
Nchifukwa chake nnakunamiza
Ndimangofuna ungondilora
Ndimangofuna ukhale wanga
Ndimangofuna ungondilora
Nchifukwa chake nnakunamiza
Eeeh Eh Eeh Eeeh Eeh Eeeh
Eeeh Eh Eeh Eeeh Eeh Eeeh Eeeeeeh
Ndimangofuna ungondilora
Ndimangofuna ukhale wanga
Ndimangofuna ungondilora
Nchifukwa chake nnakunamiza
Ndimangofuna ungondilora
Ndimangofuna ukhale wanga
Ndimangofuna ungondilora
Nchifukwa chake nnakunamiza