Bluetick歌词由Major star演唱,出自专辑《Bluetick》,下面是《Bluetick》完整版歌词!
Bluetick歌词完整版
Cool chick
Mi want Cool chick
Mi say Cool chick
Mi want Cool chick
Nane funa kukhala ndika Cool chick
Ndatopa kudyesedwa ma Bluetick
Everytime ndikayimba kali too busy
Ndatopa ndizinthu za bullshit
Ndati nane funa kukhala
Ndika Cool chick
Ndatopa kudyesedwa ma Bluetick
Everytime ndikayimba kali too busy
Ndatopa ndizinthu za bullshit
Ma four, PA door, ndakayimbila call
Kati uyimbebe panopa sindili bho
Ine phe ma seven
Ndakawuza kandipeze
Kati mmmh Bae
Inetu nde sinageze
Ndati ndikubwela konko
Ndikutengele ku dinner
Kati mmmh hun
Ndiganize Kaye mwina
Ndati ukufuna
Banja kapena chatha
Kapena mantha
Mmxii ukundithera data
Is over know
Chifukwa ndeno sizoona no
Man monga simukuonano
Nde ndangotopano
Zachikondi zangochokano
Ndimangodula phone
Nkugonano gona know
Nane funa kukhala
Ndika Cool chick
Ndatopa kudyesedwa ma Bluetick
Everytime ndikayimba kali too busy
Ndatopa ndizinthu za bullshit
Ndati nane funa kukhala
Ndika Cool chick
Ndatopa kudyesedwa ma Bluetick
Everytime ndikayimba kali too busy
Ndatopa ndizinthu za bullshit
Oh eya
Ngakhale zaine amanyozela eya
Komabe Kumbali
Amandigomela eya
After mene
Amandipopela eya
Ine nasiya kumuhopela
Ndiwazake waukape
Wachabe ineyo naaah
Zonyengelera ine
Ndi nah sinkunama
Ndiwazake waukape
Wachabe ineyo naaah
Zonyengelera ine
Ndi nah sinkunama
Chama ten know
Kufika padeni know
Kutumiza text know
No reply no
No even hey no
Kundifilisa pain know
Kuchita regret know
Sizinali great know
Eish know
Mxiii