Addicted歌词由DESHO演唱,出自专辑《Tomorrow》,下面是《Addicted》完整版歌词!
Addicted歌词完整版
Jay Emm
Mtima umangoti phaphapha
Mtima umangoti
Dru..Dru..Dru..Drumz
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aah
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Coz I am addicted to you
It's not kuti iweyo mmakukaikira
Koma kungoti ineyo nnazolowela
Kukhala nawe Ah kukhala nawe
Sinfuna uzitalikila
Koma wina akangoti wakutenga
Ndzamulodza I swear
Ndzamulodza I swear
Ndzamulodza
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aaah
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Coz I am addicted to you
I am addicted to you
I am addicted to you
Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee
Pena ndimangoti Unandidyetsa mankhwala
Kulikonse ndingapite ukuganizira
Ngati ndiwe mowa ayi singakusiye
Ngati ndiwe chamba ayi undipengetsa
Koma utangoti lero chatha
Aah singalore ine Aah singalore ine
Ndati singalore
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aaah
Mtima umangoti phaphapha Aaaaah
Coz I am addicted to you
I am addicted to you
I am addicted to you
Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee
Dru....Dru....Dru...
Ukangoti wachoka wee
Wachoka wee
Ukangoti wasuntha wee
Wasuntha wee
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Mtima umangoti phaphapha Aaaah
Coz I am addicted to you
I am addicted to you
I am addicted to you
Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee....Ayeee