Kwa Ena歌词由Big C Uncle Big演唱,出自专辑《Kwa Ena》,下面是《Kwa Ena》完整版歌词!
Kwa Ena歌词完整版
Aaaaaa
Big C
Uncle, Biggie
Ngati anthu ena ake amakukonda
Zindikira ena ake sakufuna
Ngati ena sangakhale opanda iwe
Kuli ena ati alibe ntchito nawe
Dziko lonse silingamakambe za iweee
Udzasoweka umunthu
Keep focusing miyendo
Yako on the wayyyy
Pang'ono pang'ono tiyenda
Ine zikundimvekera normal
Kundikonda kumanja
Kumazeleku ndi chidani
Ine ndati sindikhudwapo
Ndikapanda kumveka izo
Ndizoona ndine ndani
Ndikuvomeleza Ndine opanda
Ntchito koma mbali ina
Anthu ena bow for me ;
Akukhomelera akupondeleza
Ndikuchipanga reject
With a big no, nooo
Ndine kapolo wanu
Ndili master kwa eeeena
Ndine mfiti kwanu
Ndili christ kwa eeeena
Ndili worst kwanu
Ndili best kwa eeeena
Ndine mphawi kwanu
Olemela kwa eeeena
Ndine wantchito
Wanu boss wa eeeena
Kwa eeeena, kwa eeeena
Ma ulemu tiwapansa dziko
Lina akugwira ya matope
Ndiwa Satanic kwanu
Iwo awona Eliya
Chonde msayambane
Ndichonyasa nkhope kwanu
Mwini wake ndona queen
Ndikudzamuveka mphete
Ukulamulira kwanu
Kwinaku akakukhapa
Oooh Lord have mercy
Iwo, bakuchelesula
Mata wati Pala
Waniona nkhubabokozga
Aaaa Bakuchita kutituma
Navambula fundo uwo kuwathokoza
Beauty in the eyes of beholder
Tose not tingatemwa hona
Chili worst kwa ena ndi
Chomwecho chimakhala
Best kwa enawo
Ndine kapolo wanu
Ndili master kwa eeeena
Ndine mfiti kwanu
Ndili christ kwa eeeena
Ndili worst kwanu
Ndili best kwa eeeena
Ndine mphawi kwanu
Olemela kwa eeeena
Ndine wantchito
Wanu boss wa eeeena
Kwa eeeena, kwa eeeena
Ndine kapolo wanu
Ndili master kwa eeeena
Ndine mfiti kwanu
Ndili christ kwa eeeena
Ndili worst kwanu
Ndili best kwa eeeena
Ndine mphawi kwanu
Olemela kwa eeeena
Ndine wantchito
Wanu boss wa eeeena
Kwa eeeena, kwa eeeena