Mwatchona歌词由DESHO演唱,出自专辑《Tomorrow》,下面是《Mwatchona》完整版歌词!
Mwatchona歌词完整版
Aaah Aaah
Desho Desho
Jay Emm
Kuno kumudzi munachokako inu nkalekale
Zoti tili ndi m'bale mpaka tiyiwale
Ngakhale ya sopo akuti simutumizako
Zoti muli ndi abale munayiwalako
Mmene munapitira or Fon simuyankha
Chonsecho pa whatsapp mmakhala daily
Chonsecho pa Facebook mmakhala daily
Koma komwe muliliko Aaaah Aaaah ayee
Achimwene mwatchona achimwene
Achimwene mwatchona achimwene
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Achimwene mwatchona achimwene
Achimwene mwatchona achimwene
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Timangomvera mwa anthumu kuti zanu zikuyenda
Timangomvera mwa anthumu kuti zanu zikutheka
Tinamvaso akuti munakwatira
Tinamvaso akuti muli ndi ana
Koma komwe muliliko ndi muliyenda
Komwe muliliko ndi muliyenda
Pajatu mthengo inu mdalaka njoka
Kwanu ndi konkuno
Inuyo mudzatipeza Ayeee
Achimwene mwatchona achimwene
Achimwene mwatchona achimwene
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Achimwene mwatchona achimwene
Achimwene mwatchona achimwene
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Drum
Drum
Drum
Drums
Achimwene mwatchona achimwene
Achimwene mwatchona achimwene
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Achimwene mwatchona achimwene
Achimwene mwatchona achimwene
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
Kaya mdzabwerako(Kaya Kaya)
(Kaya Kaya)
(Kaya kaya)